1 Mafumu 18:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ahabu anapitadi kukadya ndi kukamwa. Koma Eliya anapita pamwamba pa phiri la Karimeli. Ndiyeno anakhala chogwada+ ataika nkhope yake pakati pa mawondo ake.+
42 Ahabu anapitadi kukadya ndi kukamwa. Koma Eliya anapita pamwamba pa phiri la Karimeli. Ndiyeno anakhala chogwada+ ataika nkhope yake pakati pa mawondo ake.+