Ezekieli 18:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “‘Kodi ine ndimasangalala ndi imfa ya munthu aliyense wochimwa?+ Kodi sindisangalala kuti munthu wochimwayo abwerere kusiya njira zakezo ndi kukhalabe ndi moyo?’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
23 “‘Kodi ine ndimasangalala ndi imfa ya munthu aliyense wochimwa?+ Kodi sindisangalala kuti munthu wochimwayo abwerere kusiya njira zakezo ndi kukhalabe ndi moyo?’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.