Oweruza 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Amidiyaniwo anayamba kusautsa Aisiraeli.+ Chifukwa cha kusautsidwa ndi Amidiyani kumeneku, ana a Isiraeli anadzikonzera malo apansi osungiramo zinthu m’mapiri. Anadzikonzeranso mapanga ndi malo ena ovuta kufikako kuti azithawirako.+
2 Amidiyaniwo anayamba kusautsa Aisiraeli.+ Chifukwa cha kusautsidwa ndi Amidiyani kumeneku, ana a Isiraeli anadzikonzera malo apansi osungiramo zinthu m’mapiri. Anadzikonzeranso mapanga ndi malo ena ovuta kufikako kuti azithawirako.+