Yeremiya 49:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “‘Pambuyo pake ndidzasonkhanitsa ana a Amoni+ amene anagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina,’ watero Yehova.” Yeremiya 49:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 “Ndiyeno m’masiku otsiriza+ ndidzasonkhanitsa pamodzi anthu a ku Elamu amene anagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina,”+ watero Yehova.
6 “‘Pambuyo pake ndidzasonkhanitsa ana a Amoni+ amene anagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina,’ watero Yehova.”
39 “Ndiyeno m’masiku otsiriza+ ndidzasonkhanitsa pamodzi anthu a ku Elamu amene anagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina,”+ watero Yehova.