Ezekieli 25:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndidzapereka chiweruzo m’dziko la Mowabu,+ ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.’+