Ezekieli 34:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nkhosa zanga+ zinasochera m’mapiri onse ndi m’zitunda zonse zitalizitali.+ Zinabalalika padziko lonse lapansi, ndipo panalibe wozifufuza ndi kuziyang’anayang’ana.
6 Nkhosa zanga+ zinasochera m’mapiri onse ndi m’zitunda zonse zitalizitali.+ Zinabalalika padziko lonse lapansi, ndipo panalibe wozifufuza ndi kuziyang’anayang’ana.