Hoseya 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ine ndidzakhala ngati mkango wamphamvu kwa iwo.+ Ndidzapitiriza kuwayang’ana ngati kambuku* amene wabisala m’mphepete mwa njira.+
7 Ine ndidzakhala ngati mkango wamphamvu kwa iwo.+ Ndidzapitiriza kuwayang’ana ngati kambuku* amene wabisala m’mphepete mwa njira.+