1 Mafumu 7:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 ndowa, mafosholo, mbale zolowa, ndi ziwiya zina zonse.+ Hiramu anapanga zinthu zimenezi ndi mkuwa wonyezimira. Anapangira Mfumu Solomo kuti aziike m’nyumba ya Yehova.
45 ndowa, mafosholo, mbale zolowa, ndi ziwiya zina zonse.+ Hiramu anapanga zinthu zimenezi ndi mkuwa wonyezimira. Anapangira Mfumu Solomo kuti aziike m’nyumba ya Yehova.