2 Mafumu 25:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Tsiku lililonse ankapatsidwa chakudya+ kuchokera kwa mfumuyo, masiku onse a moyo wake.