Yeremiya 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Akazi awo amasiye achuluka kwambiri pamaso panga kuposa mchenga wa kunyanja. Ndibweretsa wowononga kwa mayi ndi mnyamata, dzuwa lili paliwombo.+ Ndiwachititsa kugwidwa ndi mantha ndi kuwasokoneza mwadzidzidzi.+
8 Akazi awo amasiye achuluka kwambiri pamaso panga kuposa mchenga wa kunyanja. Ndibweretsa wowononga kwa mayi ndi mnyamata, dzuwa lili paliwombo.+ Ndiwachititsa kugwidwa ndi mantha ndi kuwasokoneza mwadzidzidzi.+