Yeremiya 7:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Wonjezerani nsembe zanu zopsereza zathunthuzo pansembe zanu zinazo ndipo muzidye nokha.+
21 “Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Wonjezerani nsembe zanu zopsereza zathunthuzo pansembe zanu zinazo ndipo muzidye nokha.+