Yeremiya 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Akazi awo amasiye achuluka kwambiri pamaso panga kuposa mchenga wa kunyanja. Ndibweretsa wowononga kwa mayi ndi mnyamata, dzuwa lili paliwombo.+ Ndiwachititsa kugwidwa ndi mantha ndi kuwasokoneza mwadzidzidzi.+ Yeremiya 48:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Wofunkha adzalowa mumzinda uliwonse+ ndipo sipadzapezeka mzinda wopulumuka.+ Zigwa ndi malo athyathyathya adzawonongedwa ndithu, izi ndi zimene Yehova wanena.
8 Akazi awo amasiye achuluka kwambiri pamaso panga kuposa mchenga wa kunyanja. Ndibweretsa wowononga kwa mayi ndi mnyamata, dzuwa lili paliwombo.+ Ndiwachititsa kugwidwa ndi mantha ndi kuwasokoneza mwadzidzidzi.+
8 Wofunkha adzalowa mumzinda uliwonse+ ndipo sipadzapezeka mzinda wopulumuka.+ Zigwa ndi malo athyathyathya adzawonongedwa ndithu, izi ndi zimene Yehova wanena.