Yeremiya 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho, Yehova wa makamu wanena kuti: “Inetu ndikuwasungunula ndipo ndiyenera kuwasanthula.+ Nanga mwana wamkazi wa anthu anga ndingamuchitirenso zotani?+
7 Choncho, Yehova wa makamu wanena kuti: “Inetu ndikuwasungunula ndipo ndiyenera kuwasanthula.+ Nanga mwana wamkazi wa anthu anga ndingamuchitirenso zotani?+