Yeremiya 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Musamakhulupirire mawu achinyengo+ ndi kunena kuti, ‘Nyumba izi ndizo kachisi wa Yehova, inde ndi kachisi wa Yehova, ndithudi ndi kachisi wa Yehova!’
4 Musamakhulupirire mawu achinyengo+ ndi kunena kuti, ‘Nyumba izi ndizo kachisi wa Yehova, inde ndi kachisi wa Yehova, ndithudi ndi kachisi wa Yehova!’