Maliro 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mu mkwiyo wake wathyola nyanga* iliyonse ya Isiraeli.+Adani athu atatiukira, iye sanatithandize.+Mkwiyo wake ukuyakirabe Yakobo ngati moto umene wawononga ponseponse.+
3 Mu mkwiyo wake wathyola nyanga* iliyonse ya Isiraeli.+Adani athu atatiukira, iye sanatithandize.+Mkwiyo wake ukuyakirabe Yakobo ngati moto umene wawononga ponseponse.+