Yeremiya 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ine ndinati: “Ndithudi, amenewa ndi anthu onyozeka. Anachita zinthu mopusa, pakuti anakana njira ya Yehova. Anakana chilamulo cha Mulungu wawo.+
4 Ine ndinati: “Ndithudi, amenewa ndi anthu onyozeka. Anachita zinthu mopusa, pakuti anakana njira ya Yehova. Anakana chilamulo cha Mulungu wawo.+