Yeremiya 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munawabzala ndipo iwo anazika mizu. Akupitirizabe kukula ndi kubala zipatso. Amakutchulani pafupipafupi, koma impso zawo zili kutali kwambiri ndi inu.+
2 Munawabzala ndipo iwo anazika mizu. Akupitirizabe kukula ndi kubala zipatso. Amakutchulani pafupipafupi, koma impso zawo zili kutali kwambiri ndi inu.+