Salimo 58:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Imene singamve mawu a munthu wamatsenga,+Ngakhale wina wanzeru ataimanga ndi mphamvu zamatsenga.+ Mlaliki 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Njoka ikaluma munthu asanaiimbire nyimbo kuti aiseweretse,+ ndiye kuti palibe phindu kwa munthu woimba ndi lilime lakeyo.
11 Njoka ikaluma munthu asanaiimbire nyimbo kuti aiseweretse,+ ndiye kuti palibe phindu kwa munthu woimba ndi lilime lakeyo.