Salimo 115:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Amene amawapanga adzafanana nawo.+Onse amene amawakhulupirira adzakhala ngati mafanowo.+