Ezekieli 24:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ntchito yakula. Ntchito yoyeretsa mphikawo ndi yotopetsa koma dzimbiri lake, lomwe ndi lambiri, silikuchoka.+ Uponyeni pamoto ndi dzimbiri lakelo.’
12 Ntchito yakula. Ntchito yoyeretsa mphikawo ndi yotopetsa koma dzimbiri lake, lomwe ndi lambiri, silikuchoka.+ Uponyeni pamoto ndi dzimbiri lakelo.’