-
Yesaya 44:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Palibe amene akuganiza mumtima mwake+ kapena amene akudziwa zinthu, kapenanso amene ali womvetsa zinthu+ kuti adzifunse kuti: “Hafu ya mtengowu ndasonkhera moto ndipo pamakala ake ndaphikapo mkate. Ndawotchanso nyama n’kudya. Koma kodi wotsalawu ndipangire chinthu chonyansa?+ Kodi zoona ndiweramire mtengo woumawu?”
-