Yeremiya 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Mawu a Yeremiya+ mwana wa Hilikiya,* mmodzi wa ansembe a ku Anatoti,+ m’dera la Benjamini.+