Miyambo 25:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 pakuti ndi bwino kuti mfumuyo ikuuze kuti: “Bwera pamwamba pano,”+ kusiyana n’kuti ikutsitse pamaso pa munthu wolemekezeka amene wamuona ndi maso ako.+ Luka 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Wina akakuitana kuphwando laukwati, usakhale pamalo olemekezeka kwambiri.+ Mwina n’kutheka kuti waitananso wina wolemekezeka kuposa iwe,
7 pakuti ndi bwino kuti mfumuyo ikuuze kuti: “Bwera pamwamba pano,”+ kusiyana n’kuti ikutsitse pamaso pa munthu wolemekezeka amene wamuona ndi maso ako.+
8 “Wina akakuitana kuphwando laukwati, usakhale pamalo olemekezeka kwambiri.+ Mwina n’kutheka kuti waitananso wina wolemekezeka kuposa iwe,