Hoseya 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwe Samariya, fano lako la mwana wa ng’ombe latayidwa.+ Mkwiyo wanga wayakira anthu ako.+ Kodi iwo adzalephera kudziyeretsa ku tchimo lawoli mpaka liti?+
5 Iwe Samariya, fano lako la mwana wa ng’ombe latayidwa.+ Mkwiyo wanga wayakira anthu ako.+ Kodi iwo adzalephera kudziyeretsa ku tchimo lawoli mpaka liti?+