1 Samueli 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu amene sanafe anakanthidwa ndi matenda a mudzi.+ Ndipo anthu a mumzindawo anayang’ana kumwamba, kulirira+ thandizo.
12 Anthu amene sanafe anakanthidwa ndi matenda a mudzi.+ Ndipo anthu a mumzindawo anayang’ana kumwamba, kulirira+ thandizo.