Salimo 40:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Onse amene akufunafuna moyo wanga kuti aufafanize+Achite manyazi ndi kuthedwa nzeru.+Amene akukondwera ndi tsoka langa abwerere ndipo anyazitsidwe.+ Salimo 109:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Amene akulimbana ndi ine avale manyazi,+Ndipo adziphimbe ndi manyaziwo ngati akudziphimba ndi malaya akunja odula manja.+ Yesaya 45:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Anthu adzachita manyazi ndipo onsewo adzanyozeka. Anthu opanga mafano adzayenda monyozeka onse pamodzi.+
14 Onse amene akufunafuna moyo wanga kuti aufafanize+Achite manyazi ndi kuthedwa nzeru.+Amene akukondwera ndi tsoka langa abwerere ndipo anyazitsidwe.+
29 Amene akulimbana ndi ine avale manyazi,+Ndipo adziphimbe ndi manyaziwo ngati akudziphimba ndi malaya akunja odula manja.+
16 Anthu adzachita manyazi ndipo onsewo adzanyozeka. Anthu opanga mafano adzayenda monyozeka onse pamodzi.+