Yeremiya 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Wokondedwa wangayo, amene ndi cholowa changa, wakhala ngati mkango kwa ine m’nkhalango ndipo wandibangulira. N’chifukwa chake ndadana naye.+
8 Wokondedwa wangayo, amene ndi cholowa changa, wakhala ngati mkango kwa ine m’nkhalango ndipo wandibangulira. N’chifukwa chake ndadana naye.+