Yeremiya 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 N’chifukwa chiyani mukukhala ngati munthu wothedwa nzeru ndiponso ngati munthu wamphamvu amene sangathe kupulumutsa anthu ake?+ Komatu inu Yehova muli pakati pathu,+ ndipo ife tatchedwa ndi dzina lanu.+ Musatisiye.
9 N’chifukwa chiyani mukukhala ngati munthu wothedwa nzeru ndiponso ngati munthu wamphamvu amene sangathe kupulumutsa anthu ake?+ Komatu inu Yehova muli pakati pathu,+ ndipo ife tatchedwa ndi dzina lanu.+ Musatisiye.