Yesaya 40:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Mulankhuleni Yerusalemu momufika pamtima.+ Muuzeni mofuula kuti ntchito yake yogwira mokakamizidwa yatha,+ ndiponso kuti zolakwa zake zalipiridwa.+ Pakuti kuchokera m’dzanja la Yehova, iye walandira malipiro okwanira a machimo ake onse.”+ Yeremiya 17:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anthu amene amandizunza achite manyazi+ koma musalole kuti ineyo ndichite manyazi.+ Anthuwo agwidwe ndi mantha aakulu koma musalole kuti ine ndigwidwe ndi mantha aakulu. Agwetsereni tsoka+ ndipo muwaphwanye kuwirikiza kawiri.+
2 “Mulankhuleni Yerusalemu momufika pamtima.+ Muuzeni mofuula kuti ntchito yake yogwira mokakamizidwa yatha,+ ndiponso kuti zolakwa zake zalipiridwa.+ Pakuti kuchokera m’dzanja la Yehova, iye walandira malipiro okwanira a machimo ake onse.”+
18 Anthu amene amandizunza achite manyazi+ koma musalole kuti ineyo ndichite manyazi.+ Anthuwo agwidwe ndi mantha aakulu koma musalole kuti ine ndigwidwe ndi mantha aakulu. Agwetsereni tsoka+ ndipo muwaphwanye kuwirikiza kawiri.+