Ezekieli 25:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Chifukwa chakuti munawomba m’manja+ ndi kuponda pansi mwamphamvu, komanso munasangalala ndi mtima wonyoza poona zimene zinachitikira dziko la Isiraeli,+ Nahumu 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Masoka ako sadzakupatsa mpata wopuma. Chilonda chako chakhala chosachiritsika.+ Kodi pali amene sunamuvutitse ndi zoipa zako nthawi zonse?+ N’chifukwa chake onse amene adzamva za iwe adzakuwombera m’manja.”+
6 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Chifukwa chakuti munawomba m’manja+ ndi kuponda pansi mwamphamvu, komanso munasangalala ndi mtima wonyoza poona zimene zinachitikira dziko la Isiraeli,+
19 Masoka ako sadzakupatsa mpata wopuma. Chilonda chako chakhala chosachiritsika.+ Kodi pali amene sunamuvutitse ndi zoipa zako nthawi zonse?+ N’chifukwa chake onse amene adzamva za iwe adzakuwombera m’manja.”+