Salimo 37:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Khala chete pamaso pa Yehova,+Ndipo umuyembekezere ndi mtima wako wonse.+Usapse mtima ndi aliyense amene zinthu zikumuyendera bwino,+Munthu amene akukwaniritsa zolinga zake zoipa.+
7 Khala chete pamaso pa Yehova,+Ndipo umuyembekezere ndi mtima wako wonse.+Usapse mtima ndi aliyense amene zinthu zikumuyendera bwino,+Munthu amene akukwaniritsa zolinga zake zoipa.+