Deuteronomo 28:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Pamenepo udzakhala chodabwitsa,+ adzakupekera mwambi+ ndi kukutonza pakati pa mitundu yonse ya anthu amene Yehova adzakupititsako. Yeremiya 6:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Anthu adzawatcha, ‘siliva wokanidwa,’+ pakuti Yehova wawakana.”+
37 Pamenepo udzakhala chodabwitsa,+ adzakupekera mwambi+ ndi kukutonza pakati pa mitundu yonse ya anthu amene Yehova adzakupititsako.