Amosi 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano mvera mawu a Yehova, ‘Kodi iwe ukundiuza kuti: “Usanenere zinthu zoipa zokhudza Isiraeli,+ ndipo usatchule mawu alionse oipa+ okhudza nyumba ya Isaki”?
16 Tsopano mvera mawu a Yehova, ‘Kodi iwe ukundiuza kuti: “Usanenere zinthu zoipa zokhudza Isiraeli,+ ndipo usatchule mawu alionse oipa+ okhudza nyumba ya Isaki”?