Yeremiya 6:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Ndakusandutsa woyesa zitsulo pakati pa anthu anga. Ndakusandutsa wofufuza mosamala ndipo udzaonetsetsa ndi kufufuza njira zawo.+
27 “Ndakusandutsa woyesa zitsulo pakati pa anthu anga. Ndakusandutsa wofufuza mosamala ndipo udzaonetsetsa ndi kufufuza njira zawo.+