2 Mafumu 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tsopano Yehova wanena kuti: “Pabedi wakwerapo sutsikapo, chifukwa umwalira ndithu.”’”+ Eliya atalankhula mawu amenewa, anachoka.
4 Tsopano Yehova wanena kuti: “Pabedi wakwerapo sutsikapo, chifukwa umwalira ndithu.”’”+ Eliya atalankhula mawu amenewa, anachoka.