Nehemiya 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho ndinayamba kuimba mlandu anthu olemekezeka+ a ku Yuda kuti: “N’chifukwa chiyani mukuchita zinthu zoipa, mpaka kuipitsa tsiku la sabata? Ezekieli 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “‘Iwe wanyoza malo anga oyera, ndipo wadetsa sabata langa.+
17 Choncho ndinayamba kuimba mlandu anthu olemekezeka+ a ku Yuda kuti: “N’chifukwa chiyani mukuchita zinthu zoipa, mpaka kuipitsa tsiku la sabata?