Ezekieli 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kumeneko ndinaonako ulemerero wa Mulungu wa Isiraeli,+ wofanana ndi zimene ndinaona kuchigwa zija.