Salimo 33:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti iye ananena, ndipo zinachitika.+Iye analamula, ndipo zinakhalapo.+