Ezekieli 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Atayamba kulankhula nane, mzimu unalowa mwa ine+ ndipo unandiimiritsa kuti ndimvetsere yemwe anali kulankhula ndi ineyo.+ Ezekieli 37:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo ndinalosera monga mmene anandiuzira ndipo mpweya unalowa mwa anthuwo. Iwo anakhala ndi moyo ndipo anaimirira.+ Anali khamu lalikulu la gulu lankhondo.
2 Atayamba kulankhula nane, mzimu unalowa mwa ine+ ndipo unandiimiritsa kuti ndimvetsere yemwe anali kulankhula ndi ineyo.+
10 Pamenepo ndinalosera monga mmene anandiuzira ndipo mpweya unalowa mwa anthuwo. Iwo anakhala ndi moyo ndipo anaimirira.+ Anali khamu lalikulu la gulu lankhondo.