Miyambo 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndayala zofunda pabedi panga. Ndayalaponso nsalu za ku Iguputo zamitundu yosiyanasiyana.+