Ezekieli 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Madera ako ali mkatikati mwa nyanja.+ Omwe anakupanga anakukongoletsa kwambiri.+ Yona 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamene munandiponya m’malo ozama, pansi penipeni pa nyanja yakuya,+Madzi amphamvu anandimiza.Mafunde anu amphamvu anadutsa pamwamba panga.+
3 Pamene munandiponya m’malo ozama, pansi penipeni pa nyanja yakuya,+Madzi amphamvu anandimiza.Mafunde anu amphamvu anadutsa pamwamba panga.+