Ezekieli 27:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amuna achikulire a ku Gebala+ ndi anthu ake aluso anali mkati mwako monga anthu omata molumikizira matabwa ako.+ Zombo zonse zapanyanja ndi oziyendetsa anali mwa iwe kuti muchite malonda ndi kusinthana zinthu.
9 Amuna achikulire a ku Gebala+ ndi anthu ake aluso anali mkati mwako monga anthu omata molumikizira matabwa ako.+ Zombo zonse zapanyanja ndi oziyendetsa anali mwa iwe kuti muchite malonda ndi kusinthana zinthu.