Levitiko 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Cholengedwa chilichonse pakati pa nyama, chimene chili ndi ziboda zogawanika zokhala ndi mpata pakati, chomwenso chimabzikula, n’chimene mungadye.+
3 Cholengedwa chilichonse pakati pa nyama, chimene chili ndi ziboda zogawanika zokhala ndi mpata pakati, chomwenso chimabzikula, n’chimene mungadye.+