Yesaya 10:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Taonani! Ambuye woona, Yehova wa makamu, akuthyola nthambi ndipo zikugwa ndi chimkokomo.+ Nthambi zitalizitali zikudulidwa, ndipo zam’mwamba zatsitsidwa.+
33 Taonani! Ambuye woona, Yehova wa makamu, akuthyola nthambi ndipo zikugwa ndi chimkokomo.+ Nthambi zitalizitali zikudulidwa, ndipo zam’mwamba zatsitsidwa.+