Ezekieli 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 M’dziko lako simudzaponda phazi la munthu+ kapena la chiweto,+ ndipo simudzakhala munthu aliyense kwa zaka 40.+
11 M’dziko lako simudzaponda phazi la munthu+ kapena la chiweto,+ ndipo simudzakhala munthu aliyense kwa zaka 40.+