Salimo 72:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti adzalanditsa wosauka amene akufuula popempha thandizo,+Komanso wosautsika ndi aliyense wopanda womuthandiza.+
12 Pakuti adzalanditsa wosauka amene akufuula popempha thandizo,+Komanso wosautsika ndi aliyense wopanda womuthandiza.+