Salimo 83:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwo anena kuti: “Tiyeni tilande malo amene Mulungu amakhalako kuti akhale athu.”+ Ezekieli 36:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Pajatu mdani wanu wakunenani kuti,+ ‘Eyaa! Tatenga ngakhale malo okwezeka akalekale+ kukhala athu!’”’+
2 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Pajatu mdani wanu wakunenani kuti,+ ‘Eyaa! Tatenga ngakhale malo okwezeka akalekale+ kukhala athu!’”’+