Yesaya 54:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Kwa kanthawi kochepa ndinakusiyiratu,+ koma ndidzakusonkhanitsa pamodzi mwachifundo chachikulu.+ Ezekieli 37:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndidzakuikirani mitsempha ndi kukupatsani mnofu. Ndidzakukutani ndi khungu ndi kuika mpweya mwa inu ndipo mudzakhala ndi moyo.+ Choncho mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’”+ Hagai 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “‘Ulemerero wa nyumba yatsopanoyi udzakhala waukulu kuposa wa nyumba yoyamba ija,’+ watero Yehova wa makamu. “‘Ndipo ndidzakhazikitsa mtendere pamalo awa,’+ watero Yehova wa makamu.”
6 Ndidzakuikirani mitsempha ndi kukupatsani mnofu. Ndidzakukutani ndi khungu ndi kuika mpweya mwa inu ndipo mudzakhala ndi moyo.+ Choncho mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’”+
9 “‘Ulemerero wa nyumba yatsopanoyi udzakhala waukulu kuposa wa nyumba yoyamba ija,’+ watero Yehova wa makamu. “‘Ndipo ndidzakhazikitsa mtendere pamalo awa,’+ watero Yehova wa makamu.”