Mateyu 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Atabatizidwa, nthawi yomweyo Yesu anavuuka m’madzimo. Pamenepo kumwamba kunatseguka,+ ndipo Yohane anaona mzimu wa Mulungu ukutsika ngati nkhunda+ kudzamutera.+ Machitidwe 7:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Koma iye, pokhala wodzazidwa ndi mzimu woyera, anayang’anitsitsa kumwamba ndi kuona ulemelero wa Mulungu ndi wa Yesu ataimirira kudzanja lamanja la Mulungu.+ Machitidwe 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 M’masomphenyawo anaona kumwamba kutatseguka,+ ndipo chinthu china chake chinali kutsika. Chinthucho chinali chooneka ngati chinsalu chachikulu chimene achigwira m’makona onse anayi n’kumachitsitsira padziko lapansi. Chivumbulutso 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndipo nditayang’ana ndinaona kumwamba kutatseguka, kenako ndinaona hatchi yoyera.+ Wokwerapo wake dzina lake linali Wokhulupirika+ ndi Woona.+ Iyeyo anali kuweruza ndi kumenya nkhondo mwachilungamo.+
16 Atabatizidwa, nthawi yomweyo Yesu anavuuka m’madzimo. Pamenepo kumwamba kunatseguka,+ ndipo Yohane anaona mzimu wa Mulungu ukutsika ngati nkhunda+ kudzamutera.+
55 Koma iye, pokhala wodzazidwa ndi mzimu woyera, anayang’anitsitsa kumwamba ndi kuona ulemelero wa Mulungu ndi wa Yesu ataimirira kudzanja lamanja la Mulungu.+
11 M’masomphenyawo anaona kumwamba kutatseguka,+ ndipo chinthu china chake chinali kutsika. Chinthucho chinali chooneka ngati chinsalu chachikulu chimene achigwira m’makona onse anayi n’kumachitsitsira padziko lapansi.
11 Ndipo nditayang’ana ndinaona kumwamba kutatseguka, kenako ndinaona hatchi yoyera.+ Wokwerapo wake dzina lake linali Wokhulupirika+ ndi Woona.+ Iyeyo anali kuweruza ndi kumenya nkhondo mwachilungamo.+