Yeremiya 30:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Inu mudzakhaladi anthu anga+ ndipo ine ndidzakhala Mulungu wanu.”+ Ezekieli 11:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 kuti azidzatsatira malamulo anga, azidzasunga zigamulo zanga ndi kuzikwaniritsa.+ Iwo adzakhaladi anthu anga+ ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo.”’+ Ezekieli 37:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iwo adzakhala muhema wanga.+ Ine ndidzakhaladi Mulungu wawo ndipo iwo adzakhala anthu anga.+
20 kuti azidzatsatira malamulo anga, azidzasunga zigamulo zanga ndi kuzikwaniritsa.+ Iwo adzakhaladi anthu anga+ ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo.”’+